2 Mafumu 17:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho Yehova anawakwiyira kwambiri Aisiraeli moti anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.
18 Choncho Yehova anawakwiyira kwambiri Aisiraeli moti anawachotsa pamaso pake.+ Sanasiye aliyense kupatulapo fuko la Yuda lokha.