-
2 Mafumu 19:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite.+
Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+
Tsopano ndizichita.+
Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+
26 Anthu okhala mʼmizindayo adzafooka.
Adzachita mantha ndiponso adzachititsidwa manyazi.
Adzakhala ngati zomera zakutchire komanso ngati udzu wanthete wobiriwira,+
Ngati udzu womera padenga umene wawauka ndi mphepo yotentha yakumʼmawa.
-