Mlaliki 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale woipa atachita zoipa maulendo 100 nʼkukhalabe ndi moyo wautali, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino, chifukwa chakuti amamuopa.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
12 Ngakhale woipa atachita zoipa maulendo 100 nʼkukhalabe ndi moyo wautali, ine ndikudziwa kuti anthu amene amaopa Mulungu woona zidzawayendera bwino, chifukwa chakuti amamuopa.+
3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,Amene mumatsatira malamulo ake olungama.* Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.* Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+