-
Yeremiya 44:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Zimene inu ndi akazi anu mwanena mwazikwaniritsadi ndi manja anu chifukwa munanena kuti: “Ife tidzakwaniritsa malonjezo athu akuti tidzapereka nsembe kwa Mfumukazi Yakumwamba* ndi kuti tidzapereka nsembe yachakumwa kwa iye.”+ Akazi inu muchitadi zimene mwalonjeza ndipo mukwaniritsadi malonjezo anu.’
-