Yesaya 55:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+ Yesaya 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+
3 Tcherani khutu lanu ndipo mubwere kwa ine.+ Mverani ndipo mudzapitiriza kukhala ndi moyo,Ndithu ine ndidzachita nanu pangano limene lidzakhalepo mpaka kalekale+Lokhudza chikondi chokhulupirika chimene ndinalonjeza Davide. Lonjezo limeneli ndi lodalirika.+
8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+