Deuteronomo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova adzachititsa kuti adani anu akugonjetseni.+ Popita kukawaukira mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa mudzadutsa njira zosiyanasiyana 7. Mafumu onse a dziko lapansi adzachita mantha akadzaona zinthu zoipa zimene zakuchitikirani.+
25 Yehova adzachititsa kuti adani anu akugonjetseni.+ Popita kukawaukira mudzadutsa njira imodzi, koma pothawa mudzadutsa njira zosiyanasiyana 7. Mafumu onse a dziko lapansi adzachita mantha akadzaona zinthu zoipa zimene zakuchitikirani.+