Yeremiya 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene anakudzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya Yuda achita. Iwo andikhumudwitsa popereka nsembe kwa Baala.”+
17 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene anakudzalani,+ wanena kuti tsoka lidzakugwerani chifukwa cha zoipa zimene a mʼnyumba ya Isiraeli ndi a mʼnyumba ya Yuda achita. Iwo andikhumudwitsa popereka nsembe kwa Baala.”+