Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+ Yeremiya 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho dziwani ndithu kuti mudzafa ndi lupanga, njala ndi mliri mʼdziko limene mukulakalaka kupita kuti muzikakhalako.”+ Yeremiya 43:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nebukadinezara adzabwera nʼkuukira dziko la Iguputo.+ Woyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri. Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo adzatengedwa kupita ku ukapolo ndipo woyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga.+
9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+
22 Choncho dziwani ndithu kuti mudzafa ndi lupanga, njala ndi mliri mʼdziko limene mukulakalaka kupita kuti muzikakhalako.”+
11 Nebukadinezara adzabwera nʼkuukira dziko la Iguputo.+ Woyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri. Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo adzatengedwa kupita ku ukapolo ndipo woyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga.+