Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+ Yeremiya 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 ‘Chifukwa ine ndidzakupulumutsa ndithu ndipo sudzaphedwa ndi lupanga. Udzapulumuka+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ akutero Yehova.” Yeremiya 43:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anatenga amuna, akazi, ana, ana aakazi a mfumu ndiponso aliyense amene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya mʼmanja mwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani.+ Anatenganso mneneri Yeremiya ndi Baruki mwana wa Neriya.
9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+
18 ‘Chifukwa ine ndidzakupulumutsa ndithu ndipo sudzaphedwa ndi lupanga. Udzapulumuka+ chifukwa chakuti wandikhulupirira,’+ akutero Yehova.”
6 Anatenga amuna, akazi, ana, ana aakazi a mfumu ndiponso aliyense amene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya mʼmanja mwa Gedaliya+ mwana wa Ahikamu,+ mwana wa Safani.+ Anatenganso mneneri Yeremiya ndi Baruki mwana wa Neriya.