2 Mafumu 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso mʼdziko lake, chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa* cha Iguputo+ mpaka kumtsinje wa Firate.+
7 Mfumu ya Iguputo sinatulukenso mʼdziko lake, chifukwa mfumu ya Babulo inali itatenga zinthu zonse za mfumu ya Iguputo,+ kuyambira kuchigwa* cha Iguputo+ mpaka kumtsinje wa Firate.+