Ezekieli 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononga magulu a anthu a ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadinezara,* mfumu ya Babulo.+
10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononga magulu a anthu a ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadinezara,* mfumu ya Babulo.+