Genesis 36:10, 11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna amene Ada mkazi wake wa Esau anabereka, komanso Reueli, mwana wamwamuna amene Basemati mkazi wake wa Esau anabereka.+ 11 Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi.+ Ezekieli 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Nditambasulanso dzanja langa nʼkulanga Edomu ndipo ndipha anthu ndi ziweto mʼdzikolo, moti ndidzalisandutsa bwinja.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga kuyambira ku Temani mpaka ku Dedani.+ Amosi 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndidzatumiza moto ku Temani,+Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za ku Bozira.’+ Obadiya 8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?
10 Mayina a ana a Esau ndi awa: Elifazi, mwana wamwamuna amene Ada mkazi wake wa Esau anabereka, komanso Reueli, mwana wamwamuna amene Basemati mkazi wake wa Esau anabereka.+ 11 Ana a Elifazi anali Temani,+ Omari, Zefo, Gatamu ndi Kenazi.+
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Nditambasulanso dzanja langa nʼkulanga Edomu ndipo ndipha anthu ndi ziweto mʼdzikolo, moti ndidzalisandutsa bwinja.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga kuyambira ku Temani mpaka ku Dedani.+
8 Yehova akuti: “Kodi pa tsiku limenelo,Sindidzawononga anthu anzeru mu Edomu,+Komanso anthu ozindikira mʼdera lamapiri la Esau?