Obadiya 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iwo adzatenga dera la Negebu ndi dera lamapiri la Esau,+Komanso dera la Sefela ndi dera la Afilisiti.+ Adzatenganso madera a Efuraimu ndi Samariya,+Ndipo Benjamini adzatenga dera la Giliyadi.
19 Iwo adzatenga dera la Negebu ndi dera lamapiri la Esau,+Komanso dera la Sefela ndi dera la Afilisiti.+ Adzatenganso madera a Efuraimu ndi Samariya,+Ndipo Benjamini adzatenga dera la Giliyadi.