7 Mofanana ndi zimenezi, anthu amʼmizinda ya Sodomu ndi Gomora komanso mizinda yozungulira ankachita chiwerewere chonyansa kwambiri ndiponso kugonana mʼnjira imene si yachibadwa.+ Anthu amenewa anapatsidwa chilango cha chiwonongeko chosatha+ ndipo ndi chitsanzo chotichenjeza.