4 Ndinamva mawu ena kuchokera kumwamba akuti: “Tulukani mwa iye anthu anga,+ ngati simukufuna kugawana naye machimo ake ndiponso ngati simukufuna kulandira nawo ina ya miliri yake.+ 5 Chifukwa machimo ake aunjikana mpaka kumwamba,+ ndipo Mulungu wakumbukira zochita zake zopanda chilungamo.+