Yeremiya 50:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa,Amene apulumuka mʼdziko la Babulo,Kuti akanene ku Ziyoni kuti Yehova Mulungu wathu akubwezera adani ake.Akuwabwezera chifukwa cha kuwonongedwa kwa kachisi wake.+
28 Kukumveka phokoso la anthu amene akuthawa,Amene apulumuka mʼdziko la Babulo,Kuti akanene ku Ziyoni kuti Yehova Mulungu wathu akubwezera adani ake.Akuwabwezera chifukwa cha kuwonongedwa kwa kachisi wake.+