Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku+ ndipo misozi ikutsika mʼmasaya ake. Pa anthu onse amene ankamukonda, palibe aliyense amene akumutonthoza.+ Anzake onse amuchitira zachinyengo+ ndipo asanduka adani ake.
2 Iye akulira kwambiri usiku+ ndipo misozi ikutsika mʼmasaya ake. Pa anthu onse amene ankamukonda, palibe aliyense amene akumutonthoza.+ Anzake onse amuchitira zachinyengo+ ndipo asanduka adani ake.