2 Mbiri 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zedekiya+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 21 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu.+ 2 Mbiri 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anagalukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inamulumbiritsa mʼdzina la Mulungu. Zedekiya anapitiriza kukhala wosamva komanso kuumitsa mtima wake ndipo anakana kubwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli. Ezekieli 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma kenako mfumu ya Yuda inapandukira mfumu ya Babulo+ potumiza amithenga ku Iguputo kuti akatenge mahatchi+ ndi gulu lalikulu la asilikali.+ Kodi zinthu zidzaiyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi angapewe chilango? Kodi angaphwanye pangano nʼkupewabe chilango?’+
13 Kuwonjezera pamenepo, Zedekiya anagalukira Mfumu Nebukadinezara+ yomwe inamulumbiritsa mʼdzina la Mulungu. Zedekiya anapitiriza kukhala wosamva komanso kuumitsa mtima wake ndipo anakana kubwerera kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli.
15 Koma kenako mfumu ya Yuda inapandukira mfumu ya Babulo+ potumiza amithenga ku Iguputo kuti akatenge mahatchi+ ndi gulu lalikulu la asilikali.+ Kodi zinthu zidzaiyendera bwino? Kodi munthu amene akuchita zinthu zimenezi angapewe chilango? Kodi angaphwanye pangano nʼkupewabe chilango?’+