-
Yeremiya 15:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Akazi awo amasiye adzachuluka kwambiri pamaso panga kuposa mchenga wakunyanja.
Ndidzawabweretsera wowononga masana, adzawononga amayi ndi anyamata.
Ndidzawachititsa kuti asokonezeke komanso kugwidwa ndi mantha mwadzidzidzi.
-