Ezekieli 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 ‘Ndiwe wodetsedwa chifukwa cha khalidwe lako lonyansa.+ Ine ndinayesa kukuyeretsa, koma sunayere chifukwa zonyansa zako sizinachoke. Sudzayera mpaka mkwiyo wanga utatha.+
13 ‘Ndiwe wodetsedwa chifukwa cha khalidwe lako lonyansa.+ Ine ndinayesa kukuyeretsa, koma sunayere chifukwa zonyansa zako sizinachoke. Sudzayera mpaka mkwiyo wanga utatha.+