1 Samueli 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Samueli anati: “Kodi Yehova amasangalala ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zina+ kuposa kumvera mawu a Yehova? Dikira ndikuuze! Kumvera kumaposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kumaposa mafuta+ a nkhosa zamphongo. Hoseya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+
22 Samueli anati: “Kodi Yehova amasangalala ndi nsembe zopsereza ndi nsembe zina+ kuposa kumvera mawu a Yehova? Dikira ndikuuze! Kumvera kumaposa nsembe,+ ndipo kumvetsera mosamala kumaposa mafuta+ a nkhosa zamphongo.
6 Chifukwa ndimakondwera ndi chikondi chokhulupirika,* osati nsembe.Ndimakondweranso ndi kudziwa Mulungu, osati nsembe zopsereza zathunthu.+