Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+ Yesaya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+ Yesaya 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero ndinafunsa kuti: “Mpaka liti, inu Yehova?” Iye anayankha kuti: “Mpaka mizinda yawo itawonongedwa nʼkukhala mabwinjaMpaka nyumba zawo zitakhala zopanda anthu okhalamoNdiponso mpaka dziko litawonongekeratu nʼkukhala bwinja.+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+
7 Dziko lanu lawonongedwa. Mizinda yanu yawotchedwa ndi moto. Alendo akudya zokolola zochokera munthaka yanu, inu mukuona.+ Lawonongedwa ngati dziko limene lalandidwa ndi adani.+
11 Atatero ndinafunsa kuti: “Mpaka liti, inu Yehova?” Iye anayankha kuti: “Mpaka mizinda yawo itawonongedwa nʼkukhala mabwinjaMpaka nyumba zawo zitakhala zopanda anthu okhalamoNdiponso mpaka dziko litawonongekeratu nʼkukhala bwinja.+