4 ‘Iwo adzafa ndi matenda oopsa+ koma palibe amene adzalire maliro awo kapena kuwaika mʼmanda. Iwo adzakhala ngati manyowa panthaka.+ Adzafa ndi lupanga ndiponso njala.+ Mitembo yawo idzakhala chakudya cha mbalame zamumlengalenga ndi zilombo zakutchire.’