Yesaya 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, ine ndi amene ndidzachitenso zinthu zodabwitsa ndi anthu awa,+Ndidzachita zodabwitsa mʼnjira yodabwitsa.Nzeru za anthu awo anzeru zidzatha,Ndipo kumvetsetsa zinthu kwa anthu awo ozindikira kudzabisika.”+
14 Choncho, ine ndi amene ndidzachitenso zinthu zodabwitsa ndi anthu awa,+Ndidzachita zodabwitsa mʼnjira yodabwitsa.Nzeru za anthu awo anzeru zidzatha,Ndipo kumvetsetsa zinthu kwa anthu awo ozindikira kudzabisika.”+