Yeremiya 30:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Kuwonongeka kwako ndi kosachiritsika.+ Ndiponso bala lako ndi losachiritsika. 13 Palibe woti akuchonderere pa mlandu wako.Palibe njira iliyonse yochiritsira bala lako. Ndipo palibe mankhwala amene angakuchiritse.
12 Yehova wanena kuti: “Kuwonongeka kwako ndi kosachiritsika.+ Ndiponso bala lako ndi losachiritsika. 13 Palibe woti akuchonderere pa mlandu wako.Palibe njira iliyonse yochiritsira bala lako. Ndipo palibe mankhwala amene angakuchiritse.