Maliro 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu akuwafuulira kuti: “Chokani! Anthu odetsedwa inu! Chokani! Chokani! Musatikhudze!” Iwo alibe pokhala ndipo akungoyendayenda. Anthu a mitundu ina akunena kuti: “Sitilola kuti amenewa azikhala ndi ife kuno.*+ Mika 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nyamukani muzipita, chifukwa malowa si opumulirako. Popeza dzikoli ndi lodetsedwa+ liwonongedwa, ndipo liwonongedwa koopsa.+
15 Anthu akuwafuulira kuti: “Chokani! Anthu odetsedwa inu! Chokani! Chokani! Musatikhudze!” Iwo alibe pokhala ndipo akungoyendayenda. Anthu a mitundu ina akunena kuti: “Sitilola kuti amenewa azikhala ndi ife kuno.*+
10 Nyamukani muzipita, chifukwa malowa si opumulirako. Popeza dzikoli ndi lodetsedwa+ liwonongedwa, ndipo liwonongedwa koopsa.+