-
Salimo 136:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yamikani Mbuye wa ambuye,
Chifukwa chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale.
-
-
Yeremiya 51:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Iye ndi Mulungu amene anapanga dziko lapansi pogwiritsa ntchito mphamvu zake,
Amene anakhazikitsa dziko lapansi pogwiritsa ntchito nzeru zake+
Amenenso anatambasula kumwamba chifukwa cha kuzindikira kwake.+
16 Mawu ake akamveka,
Madzi akumwamba amachita mkokomo,
Ndipo amachititsa mitambo* kukwera kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.
Iye amachititsa kuti kukamagwa mvula mphezi zizingʼanima
Ndipo amatulutsa mphepo mʼnyumba zake zosungira.+
-