Yeremiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye akadzafunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova Mulungu wathu watichitira zinthu zonsezi?’ udzawayankhe kuti, ‘Mofanana ndi mmene munandisiyira nʼkukatumikira mulungu wachilendo mʼdziko lanu, mudzatumikiranso alendo mʼdziko limene si lanu.’”+
19 Ndiye akadzafunsa kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova Mulungu wathu watichitira zinthu zonsezi?’ udzawayankhe kuti, ‘Mofanana ndi mmene munandisiyira nʼkukatumikira mulungu wachilendo mʼdziko lanu, mudzatumikiranso alendo mʼdziko limene si lanu.’”+