4 Yehova wanena kuti,
‘Popeza Yuda anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.
Chifukwa chakuti anakana malamulo a Yehova,
Ndiponso chifukwa sanatsatire malangizo ake.+
Koma anasocheretsedwa ndi mabodza amene makolo awo ankatsatira.+