Salimo 34:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Talawani ndipo muona kuti Yehova ndi wabwino.+Wosangalala ndi munthu amene amathawira kwa iye. Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wosangalala ndi munthu amene amathandizidwa ndi Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+ Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+
5 Wosangalala ndi munthu amene amathandizidwa ndi Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+ Yesaya 26:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+
3 Anthu amene amakudalirani ndi mtima wonse* mudzawateteza.Mudzawapatsa mtendere wosatha,+Chifukwa amadalira inu.+