21 Ponena za Ahabu mwana wa Kolaya komanso Zedekiya mwana wa Maaseya, amene akulosera zabodza kwa inu mʼdzina langa,+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Anthu amenewa ndikuwapereka mʼmanja mwa Mfumu Nebukadinezara ya ku Babulo ndipo adzawapha inu mukuona.