5 Yehoyakimu+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 25 ndipo analamulira zaka 11 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova Mulungu wake.+ 6 Kenako Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo anabwera kudzamʼmanga ndi zomangira ziwiri zakopa nʼkupita naye ku Babulo.+