Yeremiya 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawachitira zimenezi chifukwa sanamvere mawu anga amene ndinawatumizira kudzera mwa atumiki anga omwe ndi aneneri, amene ndinkawatumiza mobwerezabwereza,’* akutero Yehova.+ ‘Koma inu simunamvere,’+ akutero Yehova.
19 Ndidzawachitira zimenezi chifukwa sanamvere mawu anga amene ndinawatumizira kudzera mwa atumiki anga omwe ndi aneneri, amene ndinkawatumiza mobwerezabwereza,’* akutero Yehova.+ ‘Koma inu simunamvere,’+ akutero Yehova.