Yeremiya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ponena za Aamoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna? Kodi alibe wolandira cholowa? Nʼchifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kuti akhale cholowa chake? Ndipo nʼchifukwa chiyani anthu ake akukhala mʼmizinda ya Isiraeli?”
49 Ponena za Aamoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna? Kodi alibe wolandira cholowa? Nʼchifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kuti akhale cholowa chake? Ndipo nʼchifukwa chiyani anthu ake akukhala mʼmizinda ya Isiraeli?”