2 Mbiri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Asa anakwiyira wamasomphenyayo ndipo anamuika mʼndende* popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi. Pa nthawi yomweyo, Asa anayambanso kupondereza anthu ake ena.
10 Koma Asa anakwiyira wamasomphenyayo ndipo anamuika mʼndende* popeza anamupsera mtima kwambiri chifukwa cha nkhani imeneyi. Pa nthawi yomweyo, Asa anayambanso kupondereza anthu ake ena.