Yesaya 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+Chifukwa anyalanyalaza malamulo,+Asintha malamulo+Ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.*+ Yeremiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinakulowetsani mʼdziko la minda ya zipatso,Kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino zamʼdzikolo.+ Koma inu munalowa mʼdziko langa nʼkuliipitsa.Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+
5 Dzikolo laipitsidwa ndi anthu okhalamo,+Chifukwa anyalanyalaza malamulo,+Asintha malamulo+Ndipo aphwanya pangano limene linayenera kukhalapo mpaka kalekale.*+
7 Kenako ndinakulowetsani mʼdziko la minda ya zipatso,Kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino zamʼdzikolo.+ Koma inu munalowa mʼdziko langa nʼkuliipitsa.Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+