-
Ezekieli 26:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikutumiza Nebukadinezara* mfumu ya Babulo, mfumu ya mafumu,+ kuchokera kumpoto+ kuti akaukire Turo. Iye adzapita ndi mahatchi,+ magaleta ankhondo,+ asilikali apamahatchi ndi gulu la asilikali ambiri. 8 Anthu omwe akukhala mʼmidzi yako imene ili kunja kwa mzindawu adzawapha ndi lupanga. Iye adzamanga mpanda womenyerapo nkhondo komanso malo okwera omenyerapo nkhondo kuti amenyane nawe ndipo adzakuukira ndi chishango chachikulu.
-