Yeremiya 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+ Ezekieli 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Zidzakhalanso choncho ndikadzabweretsa zilango zanga* 4+ izi: lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri+ kuti zikaphe anthu ndi ziweto mu Yerusalemu.+
9 Anthu amene adzatsale mumzindawu adzafa ndi lupanga, njala ndiponso mliri. Koma aliyense amene adzatuluke nʼkupita kukadzipereka mʼmanja mwa Akasidi amene akuzungulirani, adzakhalabe ndi moyo. Iye adzapulumutsa moyo wake.”’+
21 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Zidzakhalanso choncho ndikadzabweretsa zilango zanga* 4+ izi: lupanga, njala, zilombo zolusa zakutchire ndi mliri+ kuti zikaphe anthu ndi ziweto mu Yerusalemu.+