Levitiko 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.* Yeremiya 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Alimi ataya mtima ndipo aphimba mitu yawoChifukwa chakuti mʼdzikomo simunagwe mvula+Ndipo nthaka yangʼambikangʼambika. Amosi 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+Ndinagwetsa mvula mumzinda wina koma mumzinda wina sindinagwetse. Mvula inagwa mʼmunda umodziKoma mʼmunda wina, mmene simunagwe mvula, munauma.
19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.*
4 Alimi ataya mtima ndipo aphimba mitu yawoChifukwa chakuti mʼdzikomo simunagwe mvula+Ndipo nthaka yangʼambikangʼambika.
7 ‘Ine ndinakumanani mvula kutatsala miyezi itatu kuti mukolole.+Ndinagwetsa mvula mumzinda wina koma mumzinda wina sindinagwetse. Mvula inagwa mʼmunda umodziKoma mʼmunda wina, mmene simunagwe mvula, munauma.