Yeremiya 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ine sindinatumize aneneriwo, koma anathamanga. Ine sindinalankhule nawo, koma analosera.+ Yeremiya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako mneneri Yeremiya anauza mneneri Hananiya+ kuti: “Tamvera iwe Hananiya! Yehova sanakutume, koma iwe wachititsa anthuwa kukhulupirira zinthu zabodza.+
15 Kenako mneneri Yeremiya anauza mneneri Hananiya+ kuti: “Tamvera iwe Hananiya! Yehova sanakutume, koma iwe wachititsa anthuwa kukhulupirira zinthu zabodza.+