9 Ndidzachititsa kuti anthu a mitundu yonse padziko lapansi achite mantha akadzaona tsoka limene ndidzawabweretsere.+ Anthu adzawanyoza, adzawaona kuti ndi chitsanzo cha anthu amene akumana ndi tsoka, adzawaseka komanso kuwatemberera+ kulikonse kumene ndidzawabalalitsire.+