Yeremiya 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Azariya mwana wa Hoshaya, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu onse odzikuza anauza Yeremiya kuti: “Zimene ukunenazo ndi zabodza! Yehova Mulungu wathu sanakutume kuti udzatiuze kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko.’
2 Azariya mwana wa Hoshaya, Yohanani+ mwana wa Kareya ndi anthu onse odzikuza anauza Yeremiya kuti: “Zimene ukunenazo ndi zabodza! Yehova Mulungu wathu sanakutume kuti udzatiuze kuti, ‘Musapite ku Iguputo kuti mukakhale kumeneko.’