-
Ekisodo 34:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+ 7 Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa mibadwo masauzande,+ amakhululuka zolakwa ndi machimo,+ koma sadzalekerera wolakwa osamʼpatsa chilango.+ Amalanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za abambo awo.”+
-