Deuteronomo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Ngati mwamuna wakwatira mkazi koma mkaziyo sakumusangalatsa chifukwa wamupeza ndi vuto linalake, azimulembera kalata yothetsera ukwati+ nʼkumupatsa, ndipo azimuchotsa panyumba pake.+
24 “Ngati mwamuna wakwatira mkazi koma mkaziyo sakumusangalatsa chifukwa wamupeza ndi vuto linalake, azimulembera kalata yothetsera ukwati+ nʼkumupatsa, ndipo azimuchotsa panyumba pake.+