Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,Tikanakhala ngati Sodomu,Ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Yeremiya 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+ Yoweli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+Chifukwa mʼphiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ ngati mmene Yehova ananenera.Anthu opulumuka amene Yehova akuwaitana.”
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,Tikanakhala ngati Sodomu,Ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
3 “Kenako ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera mʼmayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+
32 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+Chifukwa mʼphiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ ngati mmene Yehova ananenera.Anthu opulumuka amene Yehova akuwaitana.”