Zekariya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amuna ndi akazi achikulire adzakhalanso mʼmabwalo a mzinda wa Yerusalemu, aliyense atanyamula ndodo mʼmanja mwake chifukwa cha ukalamba.*+
4 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Amuna ndi akazi achikulire adzakhalanso mʼmabwalo a mzinda wa Yerusalemu, aliyense atanyamula ndodo mʼmanja mwake chifukwa cha ukalamba.*+