51 Komanso Samariya+ sanachite machimo ofika ngakhale hafu ya machimo ako. Koma iwe unapitiriza kuchulukitsa zinthu zonyansa zimene unkachita kuposa abale ako, moti unachititsa kuti azichemwali ako aoneke ngati olungama chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene unkachita.+