Salimo 116:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova amateteza anthu osadziwa zambiri.+ Ndinafooka chifukwa cha nkhawa koma iye anandipulumutsa.