Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, zinthu zonsezi zikadzakuchitikirani nʼkukhala pamavuto aakulu, mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndipo mudzamvera mawu ake.+ Yesaya 55:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+ Yoweli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngʼambani mitima yanu,+ osati zovala zanu,+Ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,Chifukwa iye ndi wachifundo, wokoma mtima, wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.+Iye adzasintha maganizo okubweretserani tsoka.
30 Pamapeto pake, zinthu zonsezi zikadzakuchitikirani nʼkukhala pamavuto aakulu, mudzabwerera kwa Yehova Mulungu wanu ndipo mudzamvera mawu ake.+
7 Munthu woipa asiye njira yake+Ndipo wopweteka anzake asiye maganizo ake.Iye abwerere kwa Yehova ndipo adzamuchitira chifundo.+Abwerere kwa Mulungu wathu, chifukwa adzamukhululukira ndi mtima wonse.+
13 Ngʼambani mitima yanu,+ osati zovala zanu,+Ndipo bwererani kwa Yehova Mulungu wanu,Chifukwa iye ndi wachifundo, wokoma mtima, wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka.+Iye adzasintha maganizo okubweretserani tsoka.