Amosi 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mumagona pamabedi aminyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamipando yokhala ngati bedi,+Ndiponso mukudya nkhosa zamphongo komanso ana a ngʼombe* onenepa.+ Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+Ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamipando yokhala ngati bedi lidzatha.
4 Mumagona pamabedi aminyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamipando yokhala ngati bedi,+Ndiponso mukudya nkhosa zamphongo komanso ana a ngʼombe* onenepa.+ Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+Ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamipando yokhala ngati bedi lidzatha.
7 Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+Ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamipando yokhala ngati bedi lidzatha.